#Mavuto
Lazy Afternoon with lions Mavuto and Chika
"The most beautiful part of life's journey isn't always where we go, but who shares the journey with us."
Here's to the friends and family who make our days brighter!

#NTS #NationalTigerSanctuary #lions #mavuto #chika #lazyafternoon
November 22, 2026 at 9:15 PM
Kapena Usi akufuna u VP? – Namalomba

Mwina akadadziwa Michael Usi adakangokhala osapereka maganizo ake pa momwe adindo angathanirane ndi mavuto a zachuma omwe akuta dziko lino, chifukwa nde wangodzikalasulira moto. Woyankhulira...

https://malawi24.com/2026/11/17/kapena-usi-akufuna-u-vp-namalomba/
Kapena Usi akufuna u VP? – Namalomba
Mwina akadadziwa Michael Usi adakangokhala osapereka maganizo ake pa momwe adindo angathanirane ndi mavuto a zachuma omwe akuta dziko lino, chifukwa nde wangodzikalasulira moto. Woyankhulira boma yemweso ndi nduna yofalitsa nkhani Shadric Namalomba, wasambwadza Usi, ndipo wamuuza kuti ngati akufuna apatsidweso udindo wa wachiwiri kwa m’tsogoleri wa dziko anene. Chatsitsa dzaye nchakuti Lolemba sabata ino,...
malawi24.com
November 17, 2026 at 9:41 AM
Madobadobawa simudzawawonaso – Chisale

Nanga angalime? Ayitu, madobadobawo ntchito ndiyomweyo. Komabe, kuyambira lero lolemba akuyenera kupeza dimba poti nduna yanenetsa kuti iwaonetsa chidameta nkhanga mpala. Wachiwiri kwa...

https://malawi24.com/2026/11/16/madobadobawa-simudzawawonaso-chisale/
Madobadobawa simudzawawonaso – Chisale
Nanga angalime? Ayitu, madobadobawo ntchito ndiyomweyo. Komabe, kuyambira lero lolemba akuyenera kupeza dimba poti nduna yanenetsa kuti iwaonetsa chidameta nkhanga mpala. Wachiwiri kwa nduna yachitetezo mdziko, Norman Chisale walengeza kuti kuyambira lero lolemba, madobadoba omwe amapezeka ku maofesi a nthambi yopanga ziphaso zoyendera sadzapezekaso. Poyankhula loweruka, Chisale wati ena mwa mavuto omwe anthu akukumana nawo...
malawi24.com
November 16, 2026 at 3:55 AM
Tipaseni zaka ziwiri abale – wakukuta mano Namalomba

Ntchito yoyima ku mizere yosaka Mafuta, ganyu osaka ndalama zakunja mwa mavuto ena zipitilira kwa miyezi ina khumi pomwe Boma lakana msatsi ponena kuti...

https://malawi24.com/2026/11/13/tipaseni-zaka-ziwiri-abale-wakukuta-mano-namalomba/
Tipaseni zaka ziwiri abale – wakukuta mano Namalomba
Ntchito yoyima ku mizere yosaka Mafuta, ganyu osaka ndalama zakunja mwa mavuto ena zipitilira kwa miyezi ina khumi pomwe Boma lakana msatsi ponena kuti mavutowa adasiya ndi a Boma lomwe lapita la Malawi Congress ndipo zufunika nthawi. Nduna yofalitsa nkhani a Shadric Namalomba awuza nyumba ina yofalitsa nkhani kuti pakufunika zaka ziwiri kuti ndondomeko zomwe...
malawi24.com
November 13, 2026 at 2:55 PM
HAPPY TONGUE OUT TUESDAY from Mavuto!

ROOOAAARRR... or was that just a REALLY BIG YAWN?

Our handsome lion Mavuto is showing off his impressive pearly whites and an EXTRA-long tongue today! Apparently, being the King of the Jungle is exhausting work

#NationalTigerSanctuary #Mavuto #Lion #TOT
November 10, 2026 at 5:15 PM
HANDSOME LION… LITTLE PUMPKIN… BIG ATTITUDE!

Mavuto may be a big, handsome lion, but he's taking his job as guardian of his tiny pumpkin VERY seriously! His sister better not even THINK about getting her paws on his prized possession!

What's mine is MINE, sis!

#NationalTigerSanctuary #NTS
November 4, 2026 at 5:15 PM
しかし、アルコール摂取には問題点も伴う。

(Komabe, palinso mavuto okhudzana ndi kumwa mowa.)
November 2, 2026 at 8:48 AM
🇲🇼 Report de la réunion budgétaire : son impact sur les Malawites [Malawi 24]
Kuchedwetsa Msonkhano wa Bajeti: Zotsatira Zake kwa Anthu a ku Malawi [Malawi 24] - afropages.fr
Malawi ikukumana ndi mavuto azachuma monga kusowa kwa mafuta, kuchepa kwa ndalama zakunja komanso kukwera kwa mitengo ya zinthu.Panthawi imeneyi,
twp.ai
October 30, 2026 at 5:42 AM
🇲🇼 Report de la réunion budgétaire : son impact sur les Malawites [Malawi 24]
Kuchedwetsa Msonkhano wa Bajeti: Zotsatira Zake kwa Anthu a ku Malawi [Malawi 24] - afropages.fr
Malawi ikukumana ndi mavuto azachuma monga kusowa kwa mafuta, kuchepa kwa ndalama zakunja komanso kukwera kwa mitengo ya zinthu.Panthawi imeneyi,
twp.ai
October 30, 2026 at 5:42 AM
Kuchedwetsa Msonkhano wa Bajeti: Zotsatira Zake kwa Anthu a ku Malawi

Malawi ikukumana ndi mavuto azachuma monga kusowa kwa mafuta, kuchepa kwa ndalama zakunja komanso kukwera kwa mitengo ya...

https://malawi24.com/2026/10/29/kuchedwetsa-msonkhano-wa-bajeti-zotsatira-zake-kwa-anthu-a-ku-malawi/
Kuchedwetsa Msonkhano wa Bajeti: Zotsatira Zake kwa Anthu a ku Malawi
Malawi ikukumana ndi mavuto azachuma monga kusowa kwa mafuta, kuchepa kwa ndalama zakunja komanso kukwera kwa mitengo ya zinthu. Panthawi imeneyi, Purezidenti Peter Mutharika analamula kuti msonkhano wa Nyumba ya Malamulo wokambirana za mmene bajeti yayendera pakati pa chaka uimitsidwe. Msonkhanowu unkayenera kuyamba pa 9 Novembala 2026. Boma lati msonkhanowu waimitsidwa pofuna kusunga ndalama zothandizira...
malawi24.com
October 29, 2026 at 2:35 PM
GOOD NIGHT from Mavuto, Our Sleepy King!
Going... going... GONE!

Mavuto tried his best to keep those sleepy eyes open, but even the king of the jungle can't fight off a good catnap forever!

Sweet dreams from Mavuto and all of us at National Tiger Sanctuary!

#GoodNight #NationalTigerSanctuary
October 22, 2026 at 12:45 AM
Kwatsala nthawi pang’ono kuti mavutowa athe — Namalomba

Ngati munataya chikhulupiliro, boma likuti osapanga za nguluwe yolira msampha utaning’a, pomwe lati kwangotsala kanusu chabe kuti mavuto omwe akuta...

https://malawi24.com/2026/10/18/kwatsala-nthawi-pangono-kuti-mavutowa-athe-namalomba/
Kwatsala nthawi pang’ono kuti mavutowa athe — Namalomba
Ngati munataya chikhulupiliro, boma likuti osapanga za nguluwe yolira msampha utaning’a, pomwe lati kwangotsala kanusu chabe kuti mavuto omwe akuta dziko lino athe.Nduna yofalitsa nkhani, Shadric Namalomba wati ndiwokhudzika ndi nyengo zomwe a Malawi akudutsamo monga kusowa kwa mafuta, ndalama zakunja ndi kuvuta kwa magetsi, koma wati anthu asataye mtima pomwe wati mavutowa pompano akhala...
malawi24.com
October 18, 2026 at 4:05 AM
BEAM yapulumutsa wophunzira ku UNIMA

Patangodutsa masiku ochepa Malawi24 italemba nkhani ya Joseph Nenani Major, wophunzira wa ku University ya Malawi UNIMA yemwe amafuna kudzipha kaamba ka mavuto ndi ngongole, Mayi wa fuko,...

https://malawi24.com/2026/10/15/beam-yapulumutsa-wophunzira-ku-unima/
BEAM yapulumutsa wophunzira ku UNIMA
Patangodutsa masiku ochepa Malawi24 italemba nkhani ya Joseph Nenani Major, wophunzira wa ku University ya Malawi UNIMA yemwe amafuna kudzipha kaamba ka mavuto ndi ngongole, Mayi wa fuko, Gertrude Mutharika wadalitsa wophunzirayu.Mkazi wa mtsogoleri wa dzikoyu wati anakhudzika kwambiri atamva moyo omwe ophunzirayu amakhala kuyambira pomwe anayamba maphunziro ake mchaka choyamba.Kutsatira izi, kudzera ku Beautify...
malawi24.com
October 15, 2026 at 4:40 AM
Pano kukwera kwa zinthu ndi konverera – Namalomba

Boma lati a Malawi akuyenera kumayamika kuti pano mitengo ya katundu m'dziko muno ikukwera monverera poyelekeza ndi nthawi ya ulamuliro wa Malawi Congress...

https://malawi24.com/2026/10/10/pano-kukwera-kwa-zinthu-ndi-konverera-namalomba/
Pano kukwera kwa zinthu ndi konverera – Namalomba
Boma lati a Malawi akuyenera kumayamika kuti pano mitengo ya katundu m'dziko muno ikukwera monverera poyelekeza ndi nthawi ya ulamuliro wa Malawi Congress Party.Izi ndi malingana ndi nduna ya zofalitsa nkhani Shadric Namalomba yemwe Lachisanu amalunkhula ndi imodzi mwa nyumba zowulutsa nkhani m’dziko muno.Namalomba wati mavuto ena amene analipo muulamuliro wa MCP amakhala mbiri ya...
malawi24.com
October 10, 2026 at 4:30 AM
GOOD AFTERNOON from Mavuto! When you’re this handsome, sometimes you just sit back, enjoy the afternoon, and let the breeze do all the work on your mane. And yes... the tongue adds a little extra style!

#GoodAfternoon #Mavuto #Lion #NationalTigerSanctuary #LionLife #BigCats #SanctuaryLife
October 6, 2026 at 8:15 PM
I’m awake… I’m awake… I’m just waiting for the rest of me to get the message.

Mavuto is giving it his best effort, but that great big yawn says he may need just a few more minutes before officially starting his day!

Who else can relate to Mavuto?

#Mavuto #Lion #NationalTigerSanctuary #NTS
September 19, 2026 at 1:15 PM
Ansah claims expose communication rot — experts

Vice President Jane Ansah’s claims of being sidelined have opened a window into what political experts say is a troubling communication breakdown at the heart of...

https://malawi24.com/2026/09/15/ansah-claims-expose-communication-rot-experts/
Ansah claims expose communication rot — experts
Vice President Jane Ansah’s claims of being sidelined have opened a window into what political experts say is a troubling communication breakdown at the heart of government.Political Science Association spokesperson Mavuto Bamusi says the allegations raise questions about the relationship between the Office of the Vice President and the Office of the President and Cabinet...
malawi24.com
September 15, 2026 at 11:20 AM
Mavuto Lion ~ Today’s agenda: find a cozy spot, close your eyes, and let the afternoon drift by.

#NTS #NationalTigerSanctuary #lions #CozyVibes #sleepycat #GoodAfternoonEveryone
September 11, 2026 at 7:15 PM
Good Morning from Chika and Mavuto!

Another beautiful day is beginning here in the Ozarks, and lion siblings Chika and Mavuto are slowly waking up and taking in the morning. While Chika looks ready to see what the day has in store, it appears Mavuto may need just a few more minutes before he's
September 10, 2026 at 1:15 PM
Line-up of all my dnd pcs
Left to right: Dhalia, B-900h (Hermes for short), Mavuto, Tielo, and Vandar
February 3, 2025 at 10:41 AM
Meet Mavuto—the self-appointed protector of the family!

Born on April 1, 2016, Mavuto is a playful lion with a very important job…or at least, he thinks so! When someone is nearby, Mavuto sometimes likes to put on his best “I’m a big, bad lion” performance, making sure everyone knows he is perfect
August 26, 2026 at 5:36 PM
Good Morning from Mavuto!

A brand-new day has dawned at National Tiger Sanctuary, and Mavuto is already enjoying the peaceful morning, soaking up the sunshine before another day of adventures begins.

Just like the quote says, every sunrise is a new adventure—a fresh opportunity to appreciate the
July 13, 2026 at 1:15 PM
Sometimes the best enrichment is simply a peaceful moment. 🦁🎶

Mavuto looked completely content as he relaxed in his den area, listening to our director, Bryan, sing and play music just for him.

#NTS #NationalTigerSanctuary
June 27, 2026 at 11:15 PM
🦁🌙 Good Night from Mavuto.

After a day of watching over his kingdom, this handsome lion is ready to rest.

💙 The night belongs to dreamers and big cats.

#Mavuto #AfricanLion #NationalTigerSanctuary #GoodNight #LionLife
June 21, 2026 at 2:15 AM
Good Night from Mavuto!

After a busy day watching over his kingdom, this handsome lion is ready to rest.

💙 Even kings need their beauty sleep.

#Mavuto #AfricanLion #NationalTigerSanctuary #GoodNight #LionLife
June 20, 2026 at 1:15 AM